MASAPOTA ANoma protest against referee Scova Francisco Scova (C) got the blame from the supporter.There were a couple of concerns over refereeing decisions in Mighty Be Forward Wanderers draw against Dwangwa United on Saturday with the supporters railing at referee Francisco Scova over a disallowed goal and ruling out what the fans say was supposed to be a penalty for the Nomads as Amos Bello was brought down in the box.The teams went for a recess one goal apiece.Luka Milanzi had put the Nomads on the lead before Chifundo Tawiha equalized just after three minutes at the stroke of half time.But some controversial decisions by the ref met the wrath of a rather disappointed Nomads family.In the 19th minute of the second half, a lowly taken header after a scrappy play in the midfield saw Sadick Ibrahim set up Rafiq Namwera whose header past Dwangwa keeper Phillimon Barnet saw a short lived celebrations as Scova ruled it out on offside.As if this was not enough Scova had in the 37th minute of the second half waved play on after Bello was seen to have been brought down in the penalty box by a strenuous looking Gilbert Nkhokwe for the visiting side.In another incident Peter Wadabwa could have put the Nomads in the lead but he was ruled for an offside when he only remained with a flick to make.However supporters in the stands saw the situation their own way claiming the ref should have given the forward the spot kick for the ‘foul’.Heavily armed police officers had to come to the rescue of Scova after the match.After the match the fans flocked the stadium’s official gates where they were heard claiming to be ‘waiting to deal with Scova’.They claimed that the ref has problems with the team and therefore deliberately ruled out the  Namwera goal and did not give a ‘clear’ penalty to the side after a series of scrappy play in the second half.This forced police officers to handle the situation and they had to pick Scova in their highly secured vehicle locally known as ‘Chi Mbaula’.While some fans said a poor permanence by their players saw them fail to win against Dwangwa- a side which lacked finished power upfront and missed numerous chances others blamed it on the officiating panel.The Nomads won last week against Silver Strikers 2-1 and had to come from behind while Dwangwa collected their first point as they had lost 1 nil against league leaders Blue Eagles in their opener.The Dwangwa side plays Maxi Bullets today at Kamuzu Stadium.
WEATHER FORECAST FOR 25th APRIL 2016 WEATHER SYSTEM AND EXPECTED RESULTS: Expect generally mild to hot and partly cloudy conditions over most areas with a chance of rain over few areas of the north. This is due to the southeasterly air mass which is affecting Malawi. SHIRE VALLEY Warm with clear sky in the morning. Expect hot and partly cloudy conditions later in the day. Forecast Temperatures: Ngabu Min. 19°C and Max.34°C SOUTHERN HIGHLANDS Expect mild with clear sky conditions in the morning becoming hot and partly cloudy later in the afternoon. Forecast Temperatures: Blantyre Min 15°C and Max.30°C CENTRAL AREAS Cool to mild in the morning. Expect warm to hot and partly cloudy conditions later in the day. Forecast Temperatures: Lilongwe Min. 13°C and Max. 30°C LAKESHORE AREAS Warm in the morning. Expect hot and partly cloudy conditions with rain over few areas of northern lakeshore areas (Karonga) in the afternoon Forecast Temperatures: Mangochi Min. 18°C and Max. 33°C NORTHERN AREAS Cool in the morning. Expect warm and partly cloudy conditions with a chance of rain over very few areas mainly Chitipa later in the day. Forecast Temperatures: Mzuzu Min.13°C and Max. 25°C OUTLOOK FOR TUESDAY: Expect partly cloudy conditions over most areas and rain over few areas of the north. WINDS: South easterlies. TIMES FOR SUNSET FOR 25th APRIL, 2016 AND SUNRISE FOR 26TH APRIL, 2016 CITY SUNSET SUNRISE MZUZU 17:35 05:51 LILONGWE 17:34 05:54 BLANTYRE 17:27 05:49
Kumadera Okwera    Unduna woona za ulimi wa mthirira ndi chitukuko cha madzi wapempha anthu omwe akukhala m`madera otsika m`boma la Karonga kuti asamukire kumadera okwera.   Unduna wu wanena izi kudzera m`chikalata chomwe watulutsa  potsatira lipoti lomwe nthambi ya zanyengo  latulutsa report lomwe likuti m`bomali mugwa mvula yambiri kwa masiku asanu akudzawa yomwe ikhonza kuchitisa madzi osefukira.   Kudzera m`chikalatachi chomwe chasayinidwa ndi  mkulu woona za ulimi wa nthirila ndi chitukuko cha madzi, a Sandram Maweru, mvulayi ichititsa kuti mitsinje ya Songwe, North Rukuru komanso Lufilya  isefukire zomwe  ati zikhoza kuononga katundu  komanso anthu kutaya miyoyo. M`chigawo chakumpoto mwagwa mvula yambiri yomwe yachititsa anthu ena kutaya miyoyo yawo komanso kusowa pokhala.
M'BUSA AGWIDWA KAMBA KOGWILIRA MZIMAYI WA MISALA    Apolisi ku Dowa amanga m`busa wina yemwe ndi mzika ya dziko la Democratic Republic of Congo wa kumalo osungirako anthu othawa kwawo a Dzaleka  m’bomalo kamba komuganizira kuti adagwirila mzimayi wamisala. Ofalitsa nkhani za apolisi ku Dowa Constable Godfrey Kaponda atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati  m’busayo Emanuel Bachenezi wa zaka 28 wa Mpingo wa Integrity Family Church ku Dzaleka komweko, ndipo amachokera m`dera la Bukavu m`dziko la Democratic Republic of Congo (DRC). Iye akumuganizira kuti anagwilira mzimayi wa zaka 26 zakubadwa yemwe amachokeranso dziko la Democratic Republic of Congo m’mwezi wa October chaka chatha,ndipo pano ndi woyembekezera. “M’busayo anapita ku nyumba kwa mzimayiyu kukamupemphelera kuti achire matenda amisala . M’busa Bachengezi  adanamiza zimayiyu kuti Mulungu wamuonetsa kuti mayiyu amwe mankhwala anayi nthawi imodzi osati amodzi monga momwe adamulangizira ku chipatala”, watero Kaponda.  Izi akuti  zidachititsa kuti zimayiyu agone tulo tofa nato ndipo m’busayo adapeza mwayi womugwirila. “M’busayo adagona kunyumba ya mayiyu ndipo atafunsidwa m’mawa iye adauza mayiyo kuti amamuchotsa ziwanda  za mwamuna wake yemwe adamwalira kalekale”,watero mneneli wa a polisiyu. Poopa kumangidwa m’busayo adanamiza  mzimayiyu kuti amukwatira koma patatha masabata angapo  mayiyu adatengera nkhaniyi ku bwalo la First Grade Magistrate. “Bwaloli linati mlanduwu ndi wa pa chiweniweni ndipo m’busayu amayenera ku kumupepesa mzimayiyu”,watero Kaponda. M’busayu akuyembekezeka kukayakha mlandu wogwilirira zomwe zikusemphana ndi gawo 139 la malamulo oweruzira milandu dziko lino .    

ANA ATATU AFA KUDOWA PA NGOZI ZOSIYANASIYANA      Ana awiri ku Mponela m’boma la Dowa afa chipupa cha nyumba yomwe anagona chitawagwera. Mneneli wa apolisi ku Mponela  a Kondwani Kandiado atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati ,anawo ndi Angella Hastings wa zaka zinayi  komanso Lonjezo Hastings wa zaka zisanu ndi chimodzi  ochokera  m’mudzi mwa Chimkuwu mdera la mfumu yayikulu Chakhaza m’bomalo. Panthawiyo anawo amagona m’nyumbayo  usiku wa loweruka lapitali pamodzi ndi makolo awo. Nyumba yomwe anthuwo adagona akuti imadontha kwambiri kamba ka mvula yamphamvu yomwe imagwa kuderalo, zomwe zidachititsa kuti khoma lanyumbayo linyowe ndi kugwera banjalo. “Anawa amagona ndi makolo awo m’nyumba yomwe imadotha kamba ka mvula yambiri yomwe imagwa deralo, pakati pa usiku anthu anamva mfuwu odabwitsa kunyumbako ndipo anakapeza chipupa cha nyumba chitagwera banjalo. Anthu analitengera banjali ku chipatala koma Angella komanso Lonjezo anali atafa kale ndipo amayi komanso mwana wina anangovulala,” watero Kandiado. Ku Dowa komweko mwana wa zaka zisanu ndi chimodzi wafa, jeke lodindira fodya litamugwera pantima. Caroline Jonathan adamwalira pa chipatala cha mishoni cha madisi jekeyo atamugwera kuchokera pomwe adamuika . Panthawiyi mwanayo amasewera ndi amzake. Caroline Jonathan amachokera m'mudzi mwa Malenga mfumu yaikulu Chakhaza bomalo.    
Next PostNewer Posts Previous PostOlder Posts Home